|
|
Atlas-country
|
Malawi
|
|
|
|
|
Malaŵi Malawi
|
|
|
Chi-Chewa
|
Malaŵi - Dziko la Malaŵi
Dziko la Malaŵi lomwe kale linkatchulidwa kuti Nyasaland, ndi dziko la demokilase lomwe lili ndi anthu ambiri ndipo lili cha ku m’mwera kwa Africa. Dzikoli linayandikana ndi Zambia cha ku madzulo, Tanzania cha ky mpoto ndi Mozambique kuzungulira kim’mawa, kummwera ndi ku madzulo. Chiyambi cha dzina loti Malawi sichidziwika bwino bwino, koma anthu ofufuza amakhulupilira kuti dzinali linachokela kwa chilankhulo cha anthu a mu dzikoli a ku chigawo cha kummwera, ndipo limatanthauza “kunyezimira kwa dzuwa pa nyanja”, mmene mbendera ya dzikoli liwonetsera.
|
English
|
Malawi - Republic of Malawi
The Republic of Malawi (formerly Nyasaland) is a democratic, densely populated country located in southeastern Africa. It has ► Zambia to the north-west, ► Tanzania to the north, and ► Mozambique surrounding it on the east, south, and west. The origin of the name Malawi remains unclear; it is held to be either derived from that of southern tribes, or noting the "glitter of the sun rising across the lake" (as seen in its flag).
|
|
|
Short name
|
Malawi
|
Official name
|
Republic of Malawi
|
Status
|
Independent country since 1964
|
Location
|
Southern Africa
|
Capital
|
Lilongwe
|
Population
|
17,563,749 inhabitants
|
Area
|
118,284 square kilometres (45,670 sq mi)
|
Major languages
|
English (official), ChiChewa (national), ChiTumbuka, ChiYao
|
Major religions
|
Protestantism, Islam, Roman Catholicism, and Traditional Religions
|
More information
|
Malawi, Geography of Malawi, History of Malawi and Politics of Malawi
|
More images
|
Malawi - Malawi (Category).
|
|